Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 8/08 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2008
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi N’chiyambi cha Mavuto?
    Galamukani!—2008
  • Zokumana Nazo Kuchokera ku Tuvalu
    Nsanja ya Olonda—1988
  • Zomwe Baibulo Limanena pa Nkhani Yakusintha Kwa Nyengo Komanso Tsogolo Lathu
    Nkhani Zina
  • Zifaniziro
    Galamukani!—2014
Onani Zambiri
Galamukani!—2008
g 8/08 tsamba 1-2

Zamkatimu

August 2008

Dziko Lapansi Likutentha—Kodi Ndiye Kuti Lili pa Mavuto Aakulu?

Malipoti ambirimbiri akusonyeza kuti tikapanda kuchitapo kanthu pakali pano, vuto la kutentha kwa dziko lingasinthe nyengo kwambiri motero kuti anthufe ndi chilengedwe tingakhale pa ngozi yoopsa. Kodi zimenezi ziyenera kutidetsa nkhawa? Onani zimene maumboni akusonyeza.

3 Kodi N’chiyambi cha Mavuto?

4 Kodi Dziko Lapansi Lili pa Mavuto Aakulu?

8 Kodi Tsogolo la Dzikoli Lili M’manja mwa Ndani?

10 Mbewu ya Chimanga N’njodabwitsa

13 Kubwera kwa Matchalitchi ku Tahiti

22 Mwana wa Nyani Atalira Momvetsa Chisoni

25 Nthaka

Inapangidwadi Mwaluso

26 Zimene Achinyamata Amadzifunsa

Kodi Ndingatani Kuti Ndisagonje Poyesedwa?

29 “Tikukuthokozani Chifukwa Chokonda Kwambiri Anthu”

30 Zochitika Padzikoli

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Malangizo Othandiza Kupirira Chisoni

Chikondi Champhamvu Kuposa Mphepo Yamkuntho 16

Werengani nkhani yofotokoza mmene masoka achilengedwe anakhudzira anthu. Amene akufotokoza nkhaniyi si anthu ogweredwa tsokawo, koma anthu amene anadzipereka kwambiri kuthandiza patagwa tsoka.

Kodi Tiyenera Kugwiritsa Ntchito Mafano Polambira Mulungu? 20

Anthu ambirimbiri amagwiritsa ntchito mafano ndi zithunzi za oyera mtima kuti ziwathandize kulambira. Kodi Mlengi wathu amaona bwanji zimenezi?

[Chithunzi patsamba 2]

Chilala ku Australia

[Chithunzi patsamba 2]

Madzi osefukira ku Tuvalu

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

COVER: © Ingrid Visser/SeaPics.com; page 2: Australia: Photo by Jonathan Wood/Getty Images; Tuvalu: Gary Braasch/ZUMA Press

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena