Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 9/11 tsamba 32
  • Mmene Mungakhalire Bwenzi la Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mmene Mungakhalire Bwenzi la Mulungu
  • Galamukani!—2011
Galamukani!—2011
g 9/11 tsamba 32

Mmene Mungakhalire Bwenzi la Mulungu

● Zimenezi n’zimene kabuku ka masamba 32 kakuti Mungathe Kukhala Bwenzi la Mulungu! kamatiphunzitsa. Mitu ina yosangalatsa m’kabukuka ndi monga yakuti “Mulungu Akukuitanani Kuti Mukhale Bwenzi Lake” ndi “Mulungu Ndiye Bwenzi Labwino Koposa, Limene Mungakhale Nalo.” Kabukuka anakalemba m’njira yoti kathandize munthu amene akuwerengayo kudziwa mfundo zoyambirira za m’Baibulo.

Mutu wakuti “Mabwenzi a Mulungu Adzakhala M’paradaiso,” umafotokoza momveka bwino cholinga cha Mulungu cha dziko lapansili. Komabe, kuti tidzasangalale ndi Paradaiso amene Baibulo likulonjeza, tiyenera kudziwa kuti kodi Mulungu amafuna tizimutumikira bwanji. Mitu monga yakuti “Mmene Mungapezere Chipembedzo Choona” ndi “Kanani Chipembedzo Chonyenga!” idzakuthandizani kuti mukhale bwenzi la Mulungu ndiponso kuti Mulunguyo azikukondani. Tikukhulupirira kuti mukawerenga kabuku kameneka, muona kuti n’kothandiza.

Ngati mukufuna kabukuka komanso kuphunzira Baibulo, lembani zofunika m’mizere ili m’munsiyi ndipo tumizani ku adiresi yoyenera pa maadiresi amene ali patsamba 5 m’magazini ino.

□ Ndikupempha kuti munditumizire kabukuka.

□ Nditumizireni munthu kuti ayambe kuphunzira nane Baibulo kwaulere.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena