Mungawerengenso Nkhani zina Pawebusaiti Yathu
MAVIDIYO
‘Uthenga Wabwino Ukulalikidwa Kudziko Lililonse, Fuko Lililonse ndi Chinenero Chilichonse’
Onerani vidiyoyi kuti muone mmene a Mboni za Yehova amagwirira ntchito youza anthu mfundo zothandiza za m’Baibulo m’zinenero zambiri padziko lonse.
(Pitani pomwe palembedwa kuti, MABUKU > MAVIDIYO)