Mungawerengenso Nkhani Zina Pawebusaiti Yathu
NKHANI
Kodi nthawi zonse mumati mukamakambirana ndi mwamuna kapena mkazi wanu zimangothera m’mikangano? Ngati zili choncho, nkhaniyi ingakuthandizeni
(Pitani pomwe palembedwa kuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA)
MAVIDIYO
N’chifukwa chiyani n’zomveka kukhulupirira kuti tinachita kulengedwa?
(Pitani pomwe palembedwa kuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)