Mungawerengenso Nkhani Zina Pawebusaiti Yathu
ANA
Khalani Bwenzi la Yehova—Uzikhala Waukhondo
Ana angaphunzire mfundo zofunika kwambiri m’mavidiyowa.
(Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)
KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO
Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Khirisimasi?
Mukhoza kudabwa mukawerenga mmene miyambo 6 ya Khirisimasi inayambira.
(Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO > Zikondwerero)