Mungawerengenso Nkhani Zina Pawebusaiti Yathu
MAVIDIYO
Kodi mumaona kuti makolo anu amakuonani ngati mwana ndipo sakulolani kuchita zinthu zina? Nanga mungatani kuti azikudalirani?
(Pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
Zimene Baibulo Limaphunzitsa
Kodi Analemba Baibulo Ndi Ndani?
Ngati Baibulo linalembedwa ndi anthu, kodi zingatheke bwanji kuti likhale Mawu a Mulungu?
(Pitani pamene alemba kuti MABUKU > MAVIDIYO, n’kudina pamene alemba kuti “Baibulo”)