Mungawerengenso Nkhani Zina Pawebusaiti Yathu
KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO
Malangizo anzeru opezeka m’Baibulo athandiza kale anthu mamiliyoni ambiri kuti akhale ndi mabanja osangalala.
(Pitani pomwe palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO)
MAVIDIYO
MMENE MOYO UNAYAMBIRA
Monica Richardson: Dokotala Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake
Zimene anaphunzira zokhudza zomwe zimachitika mwana akatsala pang’ono kubadwa zinamuthandiza kudziwa kuti zamoyo zinachita kulengedwa.
(Pitani pamene palembedwa kuti MABUKU > MAVIDIYO, pachigawo cha “Zochitika pa Moyo wa Anthu Ena”)