Mungawerengenso Nkhani Zina Pawebusaiti Yathu
A Mboni za Yehova ndi odziwika bwino padziko lonse kuti amakana kupita kunkhondo. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake sitipita kunkhondo.
(Pitani pomwe palembedwa kuti ZOKHUDZA IFEYO > MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI)
M’mayiko ambirimbiri, a Mboni za Yehova amathandiza anthu amene ali m’mavuto.
(Pitani pomwe palembedwa kuti ZOKHUDZA IFEYO > ZIMENE TIMACHITA)