Mfundo Zothandiza Amene Aferedwa
Na. 3 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa.Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka ndalama zothandizira pa ntchito yolalikira, pitani pawebusaiti yathu ya jw.org/ny. Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulako ngati tasonyeza Baibulo lina.