Mungatani Kuti Muchepetse Nkhawa?
Na. 1 2020
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka ndalama zothandizira pa ntchito yolalikira, pitani pa donate.jw.org. Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulako ngati tasonyeza Baibulo lina.