Zam’katimu
TSAMBA PHUNZIRO
5 1 Kulankhula Mawu Okondweretsa a Choonadi
9 2 Sukulu ya Utumiki Wateokalase Imapindulitsa
14 3 Baibulo—Buku Lathu—Lalikulu Lophunzira
19 4 Mmene Tingaŵerengere ndi Kukumbukira
24 5 Khalani Mmvetseri Wabwino
29 6 ‘Chitani Khama Kuŵerenga Poyera’
49 10 Kukulitsa Luso Lophunzitsa
54 11 Kukhala ndi Kalankhulidwe Kabwino Tsiku ndi Tsiku
58 12 Kulankhula Kochokera m’Maganizo ndi Kulankhula Mwadzidzidzi
63 13 Kuwongolera Kamvekedwe ka Mawu ndi Kugwiritsa Ntchito Cholankhulira
69 14 Khalani Osamala Komanso Olimba
73 15 Kuwafika Pamtima Omvetsera Anu
90 18 Kuwongolera Mayankho Anu
96 19 Kugwiritsa Ntchito Sukulu Kuwongolera Utumiki Wakumunda
108 21 Mfundo Zopatsa Chidziŵitso, Zofotokozedwa Momveka Bwino
113 22 Mawu Oyamba Ogwira Mtima
116 23 Mphamvu ya Mawu ndi Kupuma
122 24 Kulozera Maganizo a Omvetsera ku Baibulo
126 25 Kuŵerenga Malemba ndi Kuwatanthauzira
130 26 Ntchito ya Kubwereza ndi Manja
133 27 Kugogomeza Mutu wa Nkhani ndi Mfundo Zazikulu
138 28 Kuyendera Limodzi ndi Omvetsera ndi Ntchito ya Notsi
142 29 Kulankhula Nkhani Mosadodoma, Mokambirana Komanso Motchula Bwino Mawu
149 30 Kulankhula Nkhani Kogwirizanika
153 31 Khutiritsani Omvetsera Anu, Lingalirani Nawo
158 32 Kugogomeza Ganizo ndi Kusinthasintha Mawu
163 33 Kuonetsa Kutengeka Mtima ndi Mzimu Waubwenzi
172 35 Kugwirizanitsa Nkhani ndi Utumiki Wakumunda
175 36 Mawu Omalizira Oyenera ndi Kusunga Nthaŵi
181 37 Kukhazikika Maganizo ndi Maonekedwe a Munthu
188 38 Kupita Kwanu Patsogolo Kuonekere
CHIDZIŴITSO: Baibulo limene tagwiritsa ntchito m’buku lino ndi Revised Nyanja (Union) Version, kusiyapo ngati tasonyeza lina. Komabe tatsatira kalembedwe ka orthography yatsopano. Pamene mawu ogwidwa atsatiridwa ndi NW, matembenuzidwewo ali a New World Translation of the Holy Scriptures—With References.