Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Kodi Moyo Uno Ndiwo Wokha Umene Ulipo?
Zikhulupiriro zambiri zofala zonena za moyo ndi imfa zasungabe mamiliyoni ambiri m’kugwidwa ndi mantha. Bukhu lino lafalitsidwa ndi chiyembekezo chakuti lidzathandiza anthu oona mtima kulandira chimasuko chimene choonandi chokha chingapereke. Likuthandizenitu kupeza chifuno cheni-cheni m’kukhala ndi moyo tsopano ndi kukhala ndi chiyembekezo chabwino kwambiri cha m’tsogolo.
—Afalitsi