Imbirani Yehova Zitamando
“Myimbireni Yehova, inu, dziko lonse lapansi. Pakuti Yehova ndiwamkulu, nayenera kulemekezedwa kwakukulu.”—Salmo 96:1, 4.
Kupeza Nyimbo Zofunika: Kaamba ka chisonyezero cha nyimbo mogwirizana ndi mutu wa nyimbo, wonani masamba anayi otsirizira.