Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Mboni za Yehova ndi Maphunziro
Kabukuka sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama pitani pa webusaiti ya www.pr418.com/ny.
Malemba m’buku lino akuchokera m’Baibulo la Revised Nyanja (Union) Version, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina. Komabe, Chinyanjacho tachilemba m’kalembedwe katsopano. Pamene tasonyeza NW, ndiye kuti lembalo lachokera m’Baibulo la New World Translation of the Holy Scriptures la 1984
Kosindikizidwa mu February 2019
Chichewa (ed-CN)
© 1995, 2002, 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania