Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja
© 1996
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA
OFALITSA
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF SOUTH AFRICA, 1 Robert Broom Drive East, Rangeview, Krugersdorp, 1739, R.S.A.
Losindikizidwa mu 2012
Bukuli sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu ama pereka mwa kufuna kwawo.
Malemba achiheberi m’buku lino akuchokera m’Baibulo la Buku Lopatulika Ndilo Mau a Mulungu, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina. Komabe, Chichewa chake tachilemba m’kalembedwe kamakono. Pamene tasonyeza NW, ndiye kuti lembalo lachokera m’Baibulo la New World Translation of the Holy Scriptures—With References.