Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Mungathe Kukhala Bwenzi la Mulungu!
Kabukuka sikogulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama zothandizira pa ntchito yolalikira, pitani pawebusaiti yathu ya www.pr418.com/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Buku Lopatulika Ndilo Mau a Mulungu, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Losindikizidwa mu January 2017
Chichewa (gf-CN)
© 2000
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania