Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Njira ya ku Moyo Wosatha—Kodi Mwaipeza?
Kabukuka sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama pitani pa webusaiti ya www.pr418.com/ny.
Malemba onse m’kabuku kano akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina
Kosindikizidwa mu 2012
Chichewa (ol-CN)
© 2002
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania