Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
‘Onani Dziko Lokoma’
Malemba onse m’kabuku kano akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
[Mapu pamasamba 2, 3]
(Onani m’kabuku kenikeni kuti mumvetse izi)
La ku Middle East
BRITAIN
SPANYA (TARISI?)
ITALIYA
GIRISI
ASIYA MINA
DZIKO LOLONJEZEDWA
IGUPTO
ITIOPIYA
ARABIA
SEBA
ASURI
BABULO
MEDIYA
PERISIYA
[Nyanja]
Nyanja ya Atlantic
Nyanja ya Mediterranean (Nyanja Yaikulu)
Nyanja Yakuda
Nyanja Yofiira
Nyanja ya Caspian
Nyanja ya Perisiya
Nyanja ya Arabiya
[Mitsinje]
Mtsinje wa Nile
Mtsinje wa Firate
Mtsinje wa Tigirisi
[Chithunzi chachikulu pamasamba 1, 36]
[Mawu a Zithunzi patsamba 3]
Kuyamikira Zithunzi: Zinthuzi zonse kupatulapo zili pamasamba 6 m’munsi, 24, ndi 25: Pictorial Archive (Near Eastern History) Est.; mapu ali pamasamba 9, 17 (kupatulapo ali m’kabokosi), 18, 19, ndi 29: Atengedwa pa mapu ololezedwa ndi Pictorial Archive (Near Eastern History) Est. and Survey of Israel