Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Dikirani!
Kodi Tidikire Chiyani?
N’chifukwa Chiyani Tikufunika Kudikira Makamaka Panopa?
Kosindikizidwa mu 2006
Kabuku kano kafalitsidwa monga mbali ya ntchito yophunzitsa anthu Baibulo yomwe ikuchitika padziko lonse. Ntchitoyi imayendetsedwa ndi zopereka zaufulu
Malemba m’kabuku kano achokera m’Baibulo la Buku Lopatulika Ndilo Mawu a Mulungu, kupatulapo ngati tasonyeza lina. Komabe, Chichewa chake tachilemba m’kalembedwe katsopano. Pamene tasonyeza NW, ndiye kuti lembalo lachokera m’Baibulo la New World Translation of the Holy Scriptures—With References
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Photo Credits: Cover: Globe: Used with permission from The George F. Cram Company, Indianapolis, Indiana; page 3: Top: SABAH ARAR/AFP/Getty Images; bottom: Godo-Foto; page 4: Food shortages: UN/DPI Photo by Eskinder Debebe; war: UN PHOTO 186705/J. Isaac; page 9: Man fishing: © Keith Ross/SuperStock; page 19: Family with cubs: Rhino and Lion Park, Gauteng, South Africa; page 20: AP Photo/Bullit Marquez