Chikuto cha Kumapeto
Kodi mungasonyeze bwanji kuti mumakonda Mulungu ndi mtima wonse?
Kodi muyenera kudalira chikumbumtima chanu ngati chili chotani?
Kodi anthu angadziwe bwanji khalidwe lanu potengera anthu amene mumacheza nawo?
Kodi mmene mumaonera ulamuliro zimachititsa kuti Mulungu azikuonani bwanji?
Kodi kutsatira malamulo a Mulungu a makhalidwe abwino n’kothandiza bwanji?
Kodi mungatani kuti muzisangalala ndi ntchito yanu?
Kodi n’chiyani chingakuthandizeni kuti muzikonda kwambiri kumvera Yehova?