Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 104
  • Tiyeni Tonse Titamande Ya

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tiyeni Tonse Titamande Ya
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Tamandani Ya
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tamandani Ya Limodzi Nane!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Tamandani Yehova Chifukwa cha Mwana Wake Wodzozedwa
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tamandani Yehova Chifukwa cha Ufumu Wake
    Imbirani Yehova
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 104

Nyimbo 104

Tiyeni Tonse Titamande Ya

Losindikizidwa

(Salimo 146:2)

1. Titamande

Ya momveka.

Amatipatsa zonse zabwino.

Titamande

Dzina lake.

Ndi wachikondi, n’ngwamphamvu zonse

Ndipo dzina lake tilengeze.

2. Titamande

Ya chifukwa

Amatimva tikamapemphera.

Dzanja lake

Ndi lamphamvu.

Amalimbikitsa ofooka.

Za mphamvu zake timalengeza.

3. Titamande

Ya mokondwa.

N’ngolungama ndi wodalirika.

Adzakonza

Zolakwika

Ndipo anthu adzadalitsidwa.

Timutamande mosangalala.

(Onaninso Sal. 94:18, 19; 145:21; 147:1; 150:2.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena