Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Kodi Zamoyo Zinachita Kulengedwa?
Kabukuka sitigulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.pr418.com/ny.
Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kasindikizidwa mu July 2017
Chichewa (lc-CN)
© 2017
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA