Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Mmene Moyo Unayambira—Mafunso 5 Ofunika Kwambiri
Kabukuka sitigulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pa www.pr418.com.
Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kasindikizidwa mu 2017
Chichewa (lf-CN)
© 2010
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA
Patsamba loyamba: Chithunzi cha molekyu ya DNA
Dziwani kuti: Zithunzi zonse za mamolekyu zangojambulidwa m’njira yoti tizitha kuziona osati ndendende mmene alili.
Photo credits: Page 4: © Petit Format/Photo Researchers, Inc.; page 5: © SPL/Photo Researchers, Inc.; page 22, tree of life: Image courtesy of Biodiversity Heritage Library; page 27, skull: © Photolibrary/age fotostock; Ida: © Martin Shields/Alamy; page 28, skulls: © Medical-on-Line/Alamy; page 29, Java Man reconstruction: © The Print Collector/Alamy