Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha
Kabukuka sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pa webusaiti ya www.pr418.com/ny
Malemba onse m’kabuku kano akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kasindikizidwa mu March 2016
Chichewa (ll-CN)
© 2011 WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA