Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Phunzitsani Ana Anu
© 2014
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Ofalitsa
Watchtower Bible and Tract Society of South Africa NPC, 1 Robert Broom Drive East, Rangeview, Krugersdorp, 1739, R.S.A.
Kosindikizidwa mu January 2014
Kabukuka sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Malemba onse m’kabuku kano akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.