Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Banja Lanu Likhoza Kukhala Losangalala
© 2014
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Ofalitsa
Printed by Watch Tower Bible and Tract society of South Africa NPC
1 Robert Broom Drive East, Rangeview, Krugersdorp, 1739, R.S.A.
Kosindikizidwa mu January 2014
Kabukuka sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.