Mungapeze Nkhani Zina Zothandiza Mabanja pa jw.org/ny
Kuti mupeze malangizo ena komanso nzeru yochokera m’Mawu a Mulungu, pitani pa webusaiti yathu. Mudzapezaponso mfundo zimene anthu ena apabanja m’mayiko osiyanasiyana anena.
Muzilemekeza mwamuna kapena mkazi wanu
Kodi mungapewe bwanji kulankhula mawu achipongwe?
Zimene mungachite kuti musamakangane
Kodi mungatani kuti muzikhululukirana?
Zimene mungachite ngati mumacheza kwambiri ndi munthu amene si mwamuna kapena mkazi wanu
Zimene mungachite ngati mkazi kapena mwamuna wanu ali ndi matenda aakulu
Mmene mungakhalire osangalala ngati mwakwatira kapena kukwatiwanso
Zimene mungachite mwana akayamba kuvuta
Zimene mungachite ngati muli ndi mwana wolumala
Muzikambirana ndi ana anu nkhani zokhudza kugonana
Kodi mungatani ngati mwana wanu wayamba kukayikira chipembedzo chanu?
Thandizani ana anu achinyamata kuti akule bwino
Mmene mungathandizire mwana wanu amene amadzivulaza mwadala
Zimene banja la ana opeza lingachite kuti lizigwirizana ndi anthu ena
Nkhani zatsopano zimaikidwa nthawi ndi nthawi.