Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Kuphunzira Malemba Tsiku ndi Tsiku—2017
Lemba la Chaka “Khulupirira Yehova ndipo chita zabwino.”—Salimo 37:3.
Kabukuka sitigulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pa webusaiti yathu ya www.pr418.com/ny.
Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kosindikizidwa mu July 2016
Chichewa (es17-CN)
© 2016
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA