Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Kuphunzira Malemba Tsiku ndi Tsiku—2019
“Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.”—Yesaya 41:10.
Kabukuka sitigulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pa webusaiti yathu ya www.pr418.com/ny.
Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kosindikizidwa mu July 2018
Chichewa (es19-CN)
© 2018
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA