Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Kuphunzira Malemba Tsiku ndi Tsiku—2021
“Mudzakhala amphamvu mukakhala osatekeseka ndi achikhulupiriro.”—Yesaya 30:15.
Kabukuka sitigulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kosindikizidwa mu July 2020
Chichewa (es21-CN)
© 2020
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA