Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • scl tsamba 87
  • Mayina Aulemu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mayina Aulemu
  • Malemba Othandiza pa Moyo wa Chikhristu
Malemba Othandiza pa Moyo wa Chikhristu
scl tsamba 87

Mayina Aulemu

Kodi Akhristu ayenera kulemekeza anthu powatchula mayina aulemu?

Yoh 5:41

  • Nkhani ya m’Baibulo yomwe ingakuthandizeni:

    • Lu 18:18, 19​—Ngakhale kuti Yesu ndi wabwino, iye anakana kutchedwa “Mphunzitsi Wabwino” ndipo ananena kuti wabwino ndi Yehova yekha basi

N’chifukwa chiyani Akhristu sagwiritsa ntchito mayina achipembedzo monga “Atate” kapena “Atsogoleri”?

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Mt 23:9-12​—Yesu ananena kuti tisamadziwike ndi mayina aulemu monga “Atate” kapena “Atsogoleri”

    • 1Ak 4:14-17​—Ngakhale kuti mtumwi Paulo anali ngati bambo wa anthu ambiri, palibe paliponse m’Baibulo pamene amatchedwa Atate Paulo kapena mayina ena

N’chifukwa chiyani Akhristu ayenera kumatchulana kuti abale ndi alongo?

Mt 23:8

Onaninso Mac 12:17; 18:18; Aro 16:1

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Yesu ananena kuti anthu amene amalambira Yehova amawaona kuti ndi abale ndi alongo ake

Kodi timadziwa bwanji kuti tingathe kutchula akuluakulu a boma, atsogoleri a ndale komanso oweruza ndi mayina awo audindo?

Aro 13:1, 7; 1Pe 2:17

  • Nkhani ya m’Baibulo yomwe ingakuthandizeni:

    • Mac 26:1, 2, 25​—Mtumwi Paulo anagwiritsa ntchito mayina audindo potchula Agiripa ndi Fesito

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena