Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • scl tsamba 31
  • Kuchitiridwa Zoipa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kuchitiridwa Zoipa
  • Malemba Othandiza pa Moyo wa Chikhristu
Malemba Othandiza pa Moyo wa Chikhristu
scl tsamba 31

Kuchitiridwa Zoipa

Kodi tingamve bwanji ngati anthu ena akutichitira zinthu zoipa?

Sl 69:20; Miy 18:14; Mla 4:1-3; Mki 2:13-16; Akl 3:21

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 2Sa 10:1-5​—Mfumu Davide anachita zinthu mokoma mtima kwambiri ndi asilikali ake ena omwe anachititsidwa manyazi ndi adani awo

    • 2Sa 13:6-19​—Tamara analira kwambiri mpaka kung’amba mkanjo wake chifukwa choti anachititsidwa manyazi Aminoni atamugwiririra

N’chiyani chimene chikusonyeza kuti Yehova amadziwa munthu wina akachitiridwa zinthu zoipa? Nanga adzachita zotani?

Yob 34:21, 22; Sl 37:8, 9; Yes 29:15, 19-21; Aro 12:17-21

Onaninso Sl 63:6, 7

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 1Sa 25:3, 14-17, 21, 32-38​—Nabala anachitira mwano Mfumu Davide ndipo zimenezi zinaika moyo wa anthu am’banja lake pangozi, kenako Yehova anamupha

    • Yer 20:1-6, 9, 11-13​—Yeremiya anafooka wansembe wina dzina lake Pasuri atamumenya n’kumuika m’matangadza, koma kenako Yehova anamulimbikitsa n’kumupulumutsa

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena