Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Kuphunzira Malemba Tsiku ndi Tsiku—2022
Lemba la Chaka “Ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.”—Salimo 34:10.
Kabukuka sitigulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kosindikizidwa mu June 2021
Chichewa (es22-CN)
© 2021
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA