Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w87 9/1 tsamba 32
  • ‘Limodzi la Mabukhu Otchuka Kwambiri M’mbiri’

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • ‘Limodzi la Mabukhu Otchuka Kwambiri M’mbiri’
  • Nsanja ya Olonda—1987
Nsanja ya Olonda—1987
w87 9/1 tsamba 32

‘Limodzi la Mabukhu Otchuka Kwambiri M’mbiri’

Kodi ndi chofalitsidwa chotani chimene mlembi wochokera ku New Zealand anali nacho m’maganizo? Kalata yake ikulongosola kuti: “Tinali osangalala kwambiri pamene tinalandira chomwe chingakhale ntchito imodzi yotchuka kwambiri m’mbiri ya kufalitsa kwamakono, bukhu lakuti Life​—How Did It Get Here? By Evolution or by Creation?

“Kufufuza komwe kunachitidwa kuchiyambi kwa ntchito yotchuka ndi ya ophunzira imeneyi kuli kotsimikizirika kuyambira pa chiyambi penipeni, ndipo njira yomveka ndi yachidule mu imene nkhani iriyonse yalongosoledwera inachititsa chifupifupi wasayansi mmodzi aliyense wa pamalo athu apakati ofufuzira sayansi ya Zamalimidwe pa Ministry of Agriculture and Fisheries kukhala wofunitsitsa kuŵerenga bukhu lonselo.”

Mungalandire kuyesedwa kofufuzidwa bwino kotheratu kwa mmene moyo unafikira pano ndipo nchiyani chimene ichi chimatanthauza kaamba ka mtsogolo mwakudzaza ndi kutumiza kapepala kotsatiraka.

Chonde tumizani, mutalipiriratu positi, bukhu la chikuto cholimba, la masamba 256 la Life​—How Did It Get Here? By Evolution or by Creation? Ndatsekeramo K20.00.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena