Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w89 4/1 tsamba 32
  • Bukhu la Nazonse la Baibulo Latsopano

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Bukhu la Nazonse la Baibulo Latsopano
  • Nsanja ya Olonda—1989
Nsanja ya Olonda—1989
w89 4/1 tsamba 32

Bukhu la Nazonse la Baibulo Latsopano

Ambiri akhala akulemba kulongosola chiyamikiro chawo kaamba ka bukhu la nazonse la Baibulo latsopano lomwe alandira. “Ndi chithandizo chabwino chotani nanga kufufuza m’mavolyumu atsopano aŵiriwa a Insight on the Scriptures!” anasonyeza kutenthedwa maganizo tero wolemba wa ku Wisconsin, U.S.A. “Iyo ndithudi iri mphatso yabwino kwambiri, yomwe ndidzaiwona kukhala ya mtengo kosatha ndi kuyesayesa kuigwiritsira ntchito mokwanira,” analemba tero mkazi wina wa ku Jamaica, West Indies.

Mavolyumu aŵiriwo a Insight on the Scriptures ali ndi chiwonkhetso cha masamba 2,560 mu zilembo zowonekera bwino, zoŵerengeka mosavuta. Zikwi za nkhani zake zandandalitsidwa mu dongosolo la alufabeti ndi zomveka. Izo zimachita ndi anthu, malo, zomera ndi moyo wa nyama, zochitika zotchuka, malongosoledwe ophiphiritsira a m’Baibulo, ndi cholembera cha zochita za Mulungu ndi mtundu wa anthu.

Nkhani makumi asanu mphambu zitatu zakulitsidwa monga mbali zapadera m’mitundu mitundu. Zambiri za izi zimaphatikizapo mamapu ndi zithunzithunzi za malo ozungulira ndi zisonyezero za nyumba zosungiramo zinthu zakale, limodzinso ndi ntchito yojambula ya luso yokonzederedwa kukuthandizani inu kuwona zolembera za Baibulo. Mbiri ya kumbuyo ya phindu ndi nsonga zolongosola zaikidwa mu unyinji wa malemba a Baibulo oposa 3,500. Mutu, lemba, ndi zilozero za malo a mapu zaphatikizidwa.

Landirani bukhu la nazonse iri la mtengo wake, la mavolyumu aŵiri mwa kutumiza kapepalaka limodzi ndi kokha K140.

Chonde tumizani, mutalipiriratu positi, bukhu la nazonse la Baibulo la mavolyumu aŵiri la Insight on the Scriptures. Ndatsekeramo K140 (Zambia). (Kunja kwa Zambia, lemberani nthambi ya kumaloko ya Watch Tower kaamba ka chidziŵitso.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena