Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w89 8/15 tsamba 32
  • Abwino Kuposa Mankhwala Aliwonse

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Abwino Kuposa Mankhwala Aliwonse
  • Nsanja ya Olonda—1989
Nsanja ya Olonda—1989
w89 8/15 tsamba 32

Abwino Kuposa Mankhwala Aliwonse

“Ndakhala ndikuvutika kwa zaka khumi ndi schizophrenia, nthenda yoipitsitsa ya maganizo,” akulemba tero mkazi kuchokera ku Ohio, U.S.A. “Chinafunikira kupatsidwa mankhwala kundithandiza kuchita nayo. Posachedwapa thupi langa lakhala likuvomereza moipa ku mankhwala, chotero chiri chovuta kwa ine kugona.

“Madzulo ena ndisanapite kukagona, ndinayamba kumvetsera ku Kingdom Melodies. Sindinakhoze kukhulupirira mmene chimenechi chinaliri chosangalatsa ndi chotonthoza. Chabwino koposa zonse, pamene ndidzuka mkati mwa usiku ndi kumverabe nyimbo zimenezo m’liwu lofeŵa ndi lotonthoza, ndimayamikira Yehova, ‘Ha, inu mudziŵadi chosangalatsa anthu anu!’ Ndipo ndimagweranso m’tulo. Kunena zowona, ali abwino kuposa mankhwala aliwonse omwe ndikanatenga.”

Nanunso mungapindule kuchokera ku kakonzedwe ka nyimbo kotonthoza kameneka. Iriyonse ya makaseti asanu ndi atatu, Kingdom Melodies Na. 1, 2, 3, 4, 5, 6, 7, ndi 8, iri kokha K20 ndipo iri ndi nthaŵi yoseŵera ya chifupifupi ora limodzi. Landirani makaseti omwe andandalitsidwa pansipa mwa kudzaza ndi kutumiza kapepala kotsatiraka.

Chonde tumizani, mutalipiriratu positi, (ma)kaseti yochongedwa pansipa.

Pa kaseti iriyonse yowodedwa, ndatsekeramo K20 (Zambia) kukwaniritsa mtengowo.

[ ] Kingdom Melodies Na. 1 [ ] Kingdom Melodies Na. 2

[ ] Kingdom Melodies Na. 3 [ ] Kingdom Melodies Na. 4

[ ] Kingdom Melodies Na. 5 [ ] Kingdom Melodies Na. 6

[ ] Kingdom Melodies Na. 7 [ ] Kingdom Melodies Na. 8

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena