Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w90 1/1 tsamba 32
  • Kupeza Chuma M’Malo Akutali

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kupeza Chuma M’Malo Akutali
  • Nsanja ya Olonda​—1990
Nsanja ya Olonda​—1990
w90 1/1 tsamba 32

Kupeza Chuma M’Malo Akutali

Kufunafuna golidi, kapena chuma china chakuthupi, kwapangitsa ambiri kupita ku malo akutali. Koma ena apita kukapeza chinachake chofunika koposa​—anthu okhala ndi mikhalidwe imene imawapanga kukhala okhumbika kwa Mulungu. Ŵerengani mu 1990 Yearbook of Jehovah’s Witnesses ponena za chuma chenicheni chimenechi.

Munthu amene anaŵerenga Yearbook yachaka chatha analemba kuti: “Nzodabwitsa kuwona mmene mumayandikirira kwa awo amene simunakumanepo nawo, ndi mmene mumagawanira nawo zisoni zawo ndi chisangalalo! Ndimalimbikitsidwa kwambiri ndi zolembera zimenezi.”

Yearbook yachaka chino iri ndi maripoti osangalatsa onena za ntchito ya Mboni za Yehova mu Colombia, Finland, ndi Suriname, limodzinso ndi chithunzi chaposachedwapa cha ntchito imene Mboni za Yehova zikuchita pa dziko lonse.

Chonde tumizani, mutalipiriratu positi, 1990 Yearbook of Jehovah’s Witnesses. Ndatumiza K16 (Zambia).

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena