Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w90 10/15 tsamba 32
  • Kodi Baibulo Liridi Mawu a Mulungu?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Baibulo Liridi Mawu a Mulungu?
  • Nsanja ya Olonda​—1990
Nsanja ya Olonda​—1990
w90 10/15 tsamba 32

Kodi Baibulo Liridi Mawu a Mulungu?

Kapena kodi Baibulo liri kokha bukhu lina lolembedwa ndi anthu? Kodi sayansi yalitsimikizira Baibulo kukhala lolakwa? Kodi zozizwitsa zosimbidwa m’Baibulo zinachitikadi?

Kalata yochokera ku Buffalo, New York, inati: “Ndangomaliza kumene kuŵerenga bukhu lakuti The Bible​—God’s Word or Man’s? Ilo silikukwaniritsa kokha kusuliza Baibulo kwa munthu komanso likupereka kulongosola komvekera kwa chifukwa chake liyenera kuvomerezedwa kukhala Mawu a Mulungu.”

Dziwonereni nokha umboniwo. Landirani bukhu labwino limeneli mwakungodzaza ndi kutumiza kapepala kotsatiraka.

Ndingakonde kulandira bukhu lachikuto cholimba lamasamba 192 lakuti The Bible​—God’s Word or Man’s? (Kunja kwa Zambia, lemberani nthambi ya Watch Tower ya kwanuko kaamba ka chidziŵitso. Onani patsamba 2.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena