Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w91 2/15 tsamba 32
  • “Zothandiza Monga Zitsogozo ku Moyo wa Tsiku ndi Tsiku”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Zothandiza Monga Zitsogozo ku Moyo wa Tsiku ndi Tsiku”
  • Nsanja ya Olonda—1991
Nsanja ya Olonda—1991
w91 2/15 tsamba 32

“Zothandiza Monga Zitsogozo ku Moyo wa Tsiku ndi Tsiku”

Zimenezo ndizimene mkazi wina wochokera ku Toronto, Canada, anatcha zofalitsidwa za Watch Tower Bible and Tract Society. “Ndimasangalala kuŵerenga izo ndi kupeza nkhanizo kukhala zachidziŵitso, zotonthoza mtima, ndipo pamwamba pa zonse, zothandiza koposa monga zitsogozo ku moyo wa tsiku ndi tsiku.”

Iye anawonjezera kuti: “Ndine womaliza maphunziro pa yunivesite, ndipo ndiyenera kuvomereza modabwitsa kuti ndaphunzira zambiri koposa kupyolera m’zofalitsidwa zanu kuposa zaka zanga zonse za maphunziro. Ndinasangalala mwapadera ndi bukhu lanu la Kupangitsa Moyo Wanu wa Banja Kukhala Wachimwemwe. Palibe zofalitsidwa zina zirizonse zomwe zakhoza kukhala ndi chisonkhezero chabwino choterocho pa moyo wanga monga mmene zachitira zanu​—izo zandithandiza ine mokulira; ndipo kaamba ka ichi ndikuyamikirani mowonadi.”

Bukhu lotchulidwa pamwambalo, Kupangitsa Moyo Wanu wa Banja Kukhala Wachimwemwe, limapereka malingaliro achindunji omwe amathandiza kuthetsa mavuto ndi kupangitsa ukwati kukhala chosangalatsa monga mmene Mlengi anafunira iwo kukhala. Kaamba ka kope lanu, dzazani ndikutumiza kapepala kotsatiraka.

Ndingakonde kulandira bukhu lachikuto cholimba lamasamba 192 la Kupangitsa Moyo Wanu wa Banja Kukhala Wachimwemwe. (Kunja kwa Zambia, lemberani nthambi ya Watch Tower yakwanuko kaamba ka chidziŵitso. Onani patsamba 2.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena