“Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano”
Lomwe liri pamwambalo ndi lonjezo lochokera kwa Mulungu limene latengedwa kukhala mutu wa brosha yochititsa nthumanzi. Kodi lonjezo limenelo limatanthauzanji kwa ife? Kodi lidzakwaniritsidwa motani, ndipo liti? Mungapeze mayankho mwakuŵerenga chofalitsidwa chokongolachi chamasamba 32. Ngati mungakonde kulandira kope, chonde dzazani ndi kutumiza kapepala kali pansipa.
Ndingakonde kulandira brosha yamasamba 32 ya “Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano.” (Kunja kwa Zambia, lemberani nthambi ya Watch Tower yakwanuko kaamba ka chidziŵitso. Onani tsamba 2.)