Kodi Ndimagazini Achipembedzo ati Omwe Amafalitsidwa Koposa? “Nsanja ya Olonda”!
Tsopano makope oposa mamiliyoni 15 a kope lirilonse la Nsanja ya Olonda amasindikizidwa m’zinenero zoposa zana limodzi. Mukhoza kulandira Nsanja ya Olonda m’chinenero chirichonse chondandalikidwa patsamba 2. Ngati mukukhumba kulandira Nsanja ya Olonda, imene imafalitsidwa kaŵiri pamwezi, chonde dzazani ndi kutumiza kapepala kotsatiraka.
Ndingakonde kuti magazini a Nsanja ya Olonda atumizidwe kunyumba kwanga. (Kunja kwa Zambia, lemberani nthambi ya Watch Tower yakwanuko kaamba ka chidziŵitso. Onani patsamba 2.)