Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w94 7/15 tsamba 32
  • Kumasuka ku Mantha Kwayandikira!

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kumasuka ku Mantha Kwayandikira!
  • Nsanja ya Olonda—1994
Nsanja ya Olonda—1994
w94 7/15 tsamba 32

Kumasuka ku Mantha Kwayandikira!

NGAKHALE kuti munthu amakhala m’mantha kwa moyo wake wonse, tingayang’ane mwachidaliro ku nthaŵi ina patsogolopa pamene Ufumu wa Mulungu mwa Kristu Yesu udzachotsa kotheratu kuvutika konse​—kuphatikizapo matenda ndi imfa. Magazini ano asonyeza zimene zifunikira kuti mupindule ndi makonzedwe achikondi a Mulungu. Ngati mungafune chidziŵitso chowonjezereka kapena kuti wina akufikireni kudzachititsa phunziro la Baibulo lapanyumba laulere kwa inu, chonde lemberani ku Watch Tower, Box 33459, Lusaka 10101, kapena ku keyala yoyenerera yondandalikidwa patsamba 2.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena