Tsamba 32
◼ Kodi kusinkhasinkha za mmene nyenyezi zinapangidwira kungakuthandizeni motani? Onani tsamba 7.
◼ Kodi mungaphunzire chiyani ponena za Mulungu mukamaona mmene mayi amakondera mwana wake? Onani tsamba 9.
◼ N’chifukwa chiyani anthu okwatirana ayenera kumamvetserana wina akamalankhula ndiponso kuzindikira mmene wina akumvera? Onani tsamba 11.
◼ Kodi Ufumu wa Mulungu n’chiyani, nanga udzachita zotani padziko lapansili? Onani tsamba 16.
◼ Kodi ndi zinthu zina ziti zimene munthu amene akudwala matenda oti afa nawo amafunikira kwambiri? Onani tsamba 28.