Tsamba 32
◼ Kodi pamoyo wanu mungadziwe bwanji njira yoyenera kutsatira? Onani tsamba 8.
◼ Kodi zinthu zimene Yesu ankaphunzitsa zinalembedwadi molondola? Onani tsamba 12.
◼ Kodi munthu wa ku Ukraine wolankhula Chijeremani, anapezeka bwanji akulalikira m’mudzi waung’ono ku Paraguay? Onani tsamba 19.
◼ Kodi matenda a dzikoli ndi ochiritsika? Onani tsamba 26.