Tsamba 32
◼ Kodi ndani amene adzamasulidwa ku helo? Onani tsamba 9.
◼ Kodi Yesu anayerekezera imfa ndi chiyani? Onani tsamba 17.
◼ Kodi ndi zinthu ziwiri ziti zimene mungachite kuti mulimbitse ukwati wanu? Onani tsamba 19 ndi 20.
◼ Kodi a Mboni za Yehova amakhulupirira kuti ndi okhawo amene adzapulumuke? Onani tsamba 28.
◼ Kodi mungamange bwanji chikhulupiriro chanu pathanthwe? Onani tsamba 29.