Tsamba 32
◼ Kodi kutsanzira Yesu kungatithandize bwanji kukhala anthu abwino komanso osangalala? Onani tsamba 4.
◼ Pali chifukwa chachikulu chiti chokhalira aukhondo kuposa kukhala ndi thanzi labwino? Onani tsamba 9.
◼ Kodi Akhristu oyambirira anathetsa bwanji vuto lawo lolalikira kwa anthu achigiriki? Onani tsamba 18.
◼ Kodi ena amachiritsa ‘mozizwitsa’ mwa mphamvu ya ndani? Onani tsamba 22.
◼ Kodi akatswiri awiri a sayansi anaona bwanji za kupeza yankho la mafunso onena za mmene chilengedwe chinayambira mwa kugwiritsa ntchito ndalama zokwana masenti 25? Onani tsamba 26.