Tsamba 32
◼ Kodi Yesu anali ndi ang’ono ake ndiponso alongo ake? Onani tsamba 6.
◼ Kodi akufa angavulaze amoyo? Onani tsamba 11.
◼ Kodi anthu angathe kupulumutsa dzikoli? Onani tsamba 18.
◼ N’chifukwa chiyani Yesu anasambitsa mapazi a atumwi ake? Onani tsamba 19.
◼ Kodi Mulungu amayankha mapemphero onse? Onani tsamba 30.