Tsamba 32
◼ Kodi Baibulo ndi losiyana m’njira ziti ndi mabuku ena opereka amalangizo? Onani tsamba 4.
◼ Werengani za mavuto komanso zinthu zochititsa chidwi zimene zinachitikira anthu omasulira Baibulo m’zinenero zamakono. Onani tsamba 8.
◼ Kodi ndi zoona kuti zipembedzo zonse zimalambira Mulungu mmodzi yekha basi? Onani tsamba 12.
◼ Werengani za m’mene munthu wina anamvera atakalalikira uthenga wabwino ku dera lozizira kwambiri, kumpoto kwa Siberia. Onani tsamba 24.
◼ Kodi n’ndani amene angakutonthozeni ndiponso kukuthandizani mukakumana ndi mavuto? Onani tsamba 28.