Tsamba 32
◼ Kodi mzimu woyera ndi munthu? Onani tsamba 4 mpaka 7.
◼ Kodi Mulungu amafuna kuti tizichita zinthu zimene sitingathe? Onani tsamba 10.
◼ Kodi n’zotheka kuti munthu amene amakhulupirira kuti kulibe Mulungu ayambe kukhulupirira Mlengi? Onani tsamba 11 mpaka 14.
◼ Kodi Mdyerekezi ndi munthu weniweni? Onani tsamba 15.
◼ Kodi tikuphunzira chiyani kwa mtumwi Petulo amene anali ndi mtima wokayikakayika ndiponso mantha? Onani tsamba 21 mpaka 25.