Zamkatimu
January 1, 2010
Kodi Mulungu Amati Chiyani Pankhani ya Kumwa Mowa?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 “Ndingomwako Botolo Limodzi Lokha”
4 Maganizo a Mulungu Pankhani ya Kumwa Mowa
6 Khalani ndi Maganizo Oyenera Pankhani ya Kumwa Mowa
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
12 Yandikirani Mulungu—Amakwaniritsa Malonjezo
24 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Anakhalabe Wokhulupirika Panthawi Yovuta
29 Zimene Owerenga Amafunsa . . .
30 Zoti Achinyamata Achite—Munthu Wodzichepetsa Ndiponso Wolimba Mtima
NKHANI ZINANSO ZIMENE ZILI M’MAGAZINI INO
13 N’chifukwa Chiyani Mulungu Anawononga Akanani?
16 Akhristu a M’nthawi ya Atumwi—Kodi Ankakhala M’nyumba Zotani?
19 Kodi Akufa Angathandize Amoyo?
22 Kodi Dziko Lapansili Lidzatha?